Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho ophunzirawo ananyamuka ndi kukachita zimene Yesu anawalamula.

  • Maliko 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho anapita ndipo anapeza bulu wamphongo atam’mangirira pakhomo, m’mphepete mwa msewu waung’ono. Chotero iwo anamasula buluyo.+

  • Luka 22:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho ananyamuka ndi kupita. Kumeneko zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Ndipo anakonza pasika kumeneko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena