Mateyu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ambiri m’khamulo anayala malaya awo akunja+ mumsewu ndipo ena anayamba kudula nthambi za mitengo n’kuziyala mumsewu.+ Maliko 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso, anthu ambiri anayala malaya awo akunja+ mumsewu, koma ena anadula zitsamba+ m’minda.+
8 Anthu ambiri m’khamulo anayala malaya awo akunja+ mumsewu ndipo ena anayamba kudula nthambi za mitengo n’kuziyala mumsewu.+