Yesaya 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzamanga misasa mokuzungulira mbali zonse kuti ndichite nawe nkhondo. Ndidzamanga mpanda wa mitengo yosongoka mokuzungulira, ndipo ndidzamanga chiunda choti ndidzamenyerepo nkhondo pomenyana nawe.+
3 Ine ndidzamanga misasa mokuzungulira mbali zonse kuti ndichite nawe nkhondo. Ndidzamanga mpanda wa mitengo yosongoka mokuzungulira, ndipo ndidzamanga chiunda choti ndidzamenyerepo nkhondo pomenyana nawe.+