Mateyu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+ Maliko 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano anafika ku Yerusalemu. Kumeneko analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa ogula ndi ogulitsa m’kachisimo. Anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndiponso mabenchi a ogulitsa nkhunda.+
12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+
15 Tsopano anafika ku Yerusalemu. Kumeneko analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa ogula ndi ogulitsa m’kachisimo. Anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndiponso mabenchi a ogulitsa nkhunda.+