Mateyu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha Yesu anati: “Inenso ndikufunsani chinthu chimodzi. Mukandiuza chinthu chimenecho, inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi:+ Maliko 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anawauza kuti: “Ndikufunsani funso limodzi. Mundiyankhe, ndipo inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zinthu zimenezi.+
24 Poyankha Yesu anati: “Inenso ndikufunsani chinthu chimodzi. Mukandiuza chinthu chimenecho, inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi:+
29 Yesu anawauza kuti: “Ndikufunsani funso limodzi. Mundiyankhe, ndipo inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zinthu zimenezi.+