Mateyu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi ubatizo wa Yohane unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?”+ Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+ Maliko 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ iye anena kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+
25 Kodi ubatizo wa Yohane unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?”+ Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+
31 Pamenepo iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ iye anena kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+