Mateyu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nangano n’chifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, woposadi mneneri.+ Luka 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+
9 Nangano n’chifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, woposadi mneneri.+
29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+