Mateyu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+ Maliko 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma nanga tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthu’ ngati?” . . . Anali kuopa khamu la anthu, chifukwa anthu onsewo anali kukhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+
26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+
32 Koma nanga tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthu’ ngati?” . . . Anali kuopa khamu la anthu, chifukwa anthu onsewo anali kukhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+