Mateyu 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero poyankha Yesu, iwo anati: “Sitikudziwa.” Nayenso anati: “Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.+ Maliko 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno poyankha kwa Yesu anangoti: “Sitikudziwa.” Nayenso Yesu anawauza kuti: “Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.”+
27 Chotero poyankha Yesu, iwo anati: “Sitikudziwa.” Nayenso anati: “Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.+
33 Ndiyeno poyankha kwa Yesu anangoti: “Sitikudziwa.” Nayenso Yesu anawauza kuti: “Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.”+