1 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse. Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+