Genesis 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yuda ataona zimenezi anauza Onani kuti: “Gona ndi mkazi wa m’bale wako ndipo uchite chokolo, kuti um’berekere ana m’bale wako.”+
8 Yuda ataona zimenezi anauza Onani kuti: “Gona ndi mkazi wa m’bale wako ndipo uchite chokolo, kuti um’berekere ana m’bale wako.”+