Yesaya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+ 2 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa anthu amenewa pamachokera anthu amene amalowerera mozemba m’mabanja,+ ndi kugwira amayi osiyanasiyana kuti akhale akapolo awo. Amayiwo amakhala ofooka, olemedwa ndi machimo, ndiponso otengeka ndi zilakolako zosiyanasiyana,+
2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+
6 Pakati pa anthu amenewa pamachokera anthu amene amalowerera mozemba m’mabanja,+ ndi kugwira amayi osiyanasiyana kuti akhale akapolo awo. Amayiwo amakhala ofooka, olemedwa ndi machimo, ndiponso otengeka ndi zilakolako zosiyanasiyana,+