Mika 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+ Mateyu 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, pa nthawiyo anthu ambiri adzapunthwa+ ndipo adzaperekana ndi kudana.+ Maliko 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso, munthu adzapereka m’bale wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake,+ ndi ana adzaukira makolo awo ndi kuwaphetsa.+ Machitidwe 7:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+
6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+
12 Komanso, munthu adzapereka m’bale wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake,+ ndi ana adzaukira makolo awo ndi kuwaphetsa.+
59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+