Mateyu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira+ kumapiri. Maliko 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Koma mukadzaona chinthu chonyansa+ chosakaza+ chitaimirira pamene sichiyenera kuima (wowerenga adzazindikire),+ pamenepo amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira kumapiri.+
14 “Koma mukadzaona chinthu chonyansa+ chosakaza+ chitaimirira pamene sichiyenera kuima (wowerenga adzazindikire),+ pamenepo amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira kumapiri.+