Zefaniya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+
17 Pamenepo ndidzasautsa mtundu wa anthu moti adzayenda ngati anthu akhungu+ chifukwa chakuti iwo achimwira Yehova.+ Magazi awo adzakhuthulidwa pansi ngati fumbi,+ ndipo matumbo awo adzakhuthulidwa pansi ngati ndowe.+