Yoweli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dziko lanjenjemera pamaso pawo ndipo kumwamba kwagwedezeka. Dzuwa ndi mwezi zada+ ndipo nyenyezi zaleka kuwala.+ Yoweli 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Ndidzachita zodabwitsa kuthambo+ ndi padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi utsi wokwera kumwamba.+
10 Dziko lanjenjemera pamaso pawo ndipo kumwamba kwagwedezeka. Dzuwa ndi mwezi zada+ ndipo nyenyezi zaleka kuwala.+
30 “Ndidzachita zodabwitsa kuthambo+ ndi padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi utsi wokwera kumwamba.+