Mateyu 24:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithu ndikukuuzani kuti m’badwo uwu+ sudzatha wonse kuchoka kufikira zinthu zonsezi zitachitika. Maliko 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndithu ndikukuuzani kuti m’badwo uwu sudzatha konse, kufikira zinthu zonsezi zitachitika.+