Mateyu 24:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka,+ koma mawu anga sadzachoka ayi.+ Maliko 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kumwamba+ ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mawu+ anga sadzachoka ayi.+ Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+