Salimo 148:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 148 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Yehova inu okhala kumwamba.+Mutamandeni inu okhala m’mwamba.+ Maliko 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wodalitsidwa ufumu ukubwerawo wa atate wathu Davide!+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”