Genesis 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ili ndi pangano limene anthu inu muyenera kulisunga, la pakati pa ine ndi inu, ngakhalenso mbewu yobwera pambuyo pa inu.+ Mwamuna aliyense pakati pa inu azidulidwa.+
10 Ili ndi pangano limene anthu inu muyenera kulisunga, la pakati pa ine ndi inu, ngakhalenso mbewu yobwera pambuyo pa inu.+ Mwamuna aliyense pakati pa inu azidulidwa.+