Levitiko 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mkazi akatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mkazi akatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba.+