Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+ 1 Timoteyo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamaso pa Mulungu, amene amasunga zinthu zonse kuti zikhalebe zamoyo, ndi pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri+ pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+
13 Pamaso pa Mulungu, amene amasunga zinthu zonse kuti zikhalebe zamoyo, ndi pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri+ pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula+