Mateyu 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akam’pachike.+ Yohane 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Pilato anatenga Yesu ndi kumukwapula.+
26 Pamenepo anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akam’pachike.+