Luka 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo anawafunsa kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti:+ “Ndinu Khristu+ wa Mulungu.”
20 Pamenepo anawafunsa kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti:+ “Ndinu Khristu+ wa Mulungu.”