Mateyu 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe. Maliko 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ansembe aakulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba.+ Yohane 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pamenepo iwo anafuulanso kuti: “Ameneyo ayi, koma Baraba!” Koma Baraba ameneyu anali wachifwamba.+
20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe.
40 Pamenepo iwo anafuulanso kuti: “Ameneyo ayi, koma Baraba!” Koma Baraba ameneyu anali wachifwamba.+