Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+ Maliko 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha, Pilato anawafunsa kuti: “Nanga uyu amene mumati ndi mfumu+ ya Ayuda, ndichite naye chiyani?”+ Yohane 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi Pilato anayesetsabe kufunafuna njira kuti amumasule. Koma Ayudawo anafuula kuti: “Mukamumasula ameneyu, ndiye kuti si inu bwenzi la Kaisara. Munthu aliyense wodziyesa yekha mfumu, ameneyo ndi wotsutsana ndi Kaisara.”+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+
12 Poyankha, Pilato anawafunsa kuti: “Nanga uyu amene mumati ndi mfumu+ ya Ayuda, ndichite naye chiyani?”+
12 Pa chifukwa chimenechi Pilato anayesetsabe kufunafuna njira kuti amumasule. Koma Ayudawo anafuula kuti: “Mukamumasula ameneyu, ndiye kuti si inu bwenzi la Kaisara. Munthu aliyense wodziyesa yekha mfumu, ameneyo ndi wotsutsana ndi Kaisara.”+