Maliko 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+ Yohane 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo anamupereka kwa iwo kuti akamupachike.+ Tsopano Yesu anakhala m’manja mwawo.
15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+