Maliko 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+ Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+
21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+
17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+