Mateyu 27:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+ Maliko 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno mawu osonyeza mlandu wake+ anawalemba pamwamba pake kuti: “Mfumu ya Ayuda.”+ Yohane 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pilato analembanso dzina laudindo ndi kuliika pamtengo wozunzikirapowo. Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+
37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+
19 Pilato analembanso dzina laudindo ndi kuliika pamtengo wozunzikirapowo. Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+