Mateyu 26:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 ndi kunena kuti: “Losera tione Khristu iwe.+ Wakumenya ndani?”+ Mateyu 27:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi anayamba kumunyoza.+ Maliko 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+
32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+