Mateyu 27:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+ Pilato analamula kuti amupatse mtembowo.+