Mateyu 27:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Yosefe anatenga mtembowo ndi kuukulunga munsalu yoyera yabwino kwambiri,+ Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+
46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+