Luka 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anatenga mitanda ya mkate isanu ija ndi nsomba ziwiri zija ndipo anayang’ana kumwamba ndi kudalitsa chakudyacho. Kenako ananyemanyema mitanda ya mkate ndi nsombazo n’kupereka kwa ophunzira kuti apatse anthuwo.+
16 Kenako anatenga mitanda ya mkate isanu ija ndi nsomba ziwiri zija ndipo anayang’ana kumwamba ndi kudalitsa chakudyacho. Kenako ananyemanyema mitanda ya mkate ndi nsombazo n’kupereka kwa ophunzira kuti apatse anthuwo.+