Levitiko 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+ Levitiko 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzisunga malamulo anga.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani monga anthu oyera.+ Salimo 119:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Odala ndi anthu osalakwitsa kanthu m’njira zawo,+Anthu amene akutsatira chilamulo cha Yehova.+
5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+