Genesis 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale akewo anachita naye kaduka,+ koma bambo ake anasunga mawuwo.+ Danieli 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Nkhani imeneyi yathera pamenepa. Tsopano ineyo Danieli, ndinachita mantha kwambiri moti ndinakhala ngati ndakomoka. Koma nkhaniyi ndinaisunga mumtima mwanga.”+ Luka 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mariya anasunga mawu onsewa ndi kuganizira tanthauzo la zimenezi mumtima mwake.+
28 “Nkhani imeneyi yathera pamenepa. Tsopano ineyo Danieli, ndinachita mantha kwambiri moti ndinakhala ngati ndakomoka. Koma nkhaniyi ndinaisunga mumtima mwanga.”+