Luka 1:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Choncho mwana uja anakulirakulira+ ndipo anali kulimba mwauzimu. Iye anali kukhala m’zipululu mpaka tsiku lakuti adzionetsere poyera kwa Isiraeli.
80 Choncho mwana uja anakulirakulira+ ndipo anali kulimba mwauzimu. Iye anali kukhala m’zipululu mpaka tsiku lakuti adzionetsere poyera kwa Isiraeli.