Yesaya 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chigwa chilichonse chikwezedwe m’mwamba,+ ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe.+ Malo okumbikakumbika asalazidwe ndipo malo azitundazitunda akhale chigwa.+
4 Chigwa chilichonse chikwezedwe m’mwamba,+ ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe.+ Malo okumbikakumbika asalazidwe ndipo malo azitundazitunda akhale chigwa.+