Mateyu 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire. Luka 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+
32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire.
29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+