Maliko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+
17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+