Mateyu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anabwera kwa Yohane ku Yorodano kuchokera ku Galileya,+ kuti iye amubatize.+ Maliko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+
9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+