Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+ Maliko 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atangovuuka m’madzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka, ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+
16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+
10 Atangovuuka m’madzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka, ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+