1 Mbiri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana amene Yekoniya anabereka ali mkaidi anali Salatiyeli,+ Mateyu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.+Salatiyeli anabereka Zerubabele.+
12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.+Salatiyeli anabereka Zerubabele.+