Rute 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano uwu ndiwo mzere wa mbadwa za Perezi:+ Perezi anabereka Hezironi,+ 1 Mbiri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+