Genesis 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Abulahamu anatcha mwana amene Sara anamuberekerayo dzina lakuti Isaki.+