-
Yohane 21:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma ophunzira enawo anabwera m’ngalawa yaing’ono akukoka ukonde wa nsomba, pakuti sanali patali kwenikweni ndi kumtunda. Anali pa mtunda wa mamita pafupifupi 90 okha.
-