Mateyu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.” Maliko 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”
40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+