Mateyu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atatero, alembi ena anang’ung’udza chamumtima kuti: “Munthu ameneyu akunyoza Mulungu.”+ Maliko 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “N’chifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyoza Mulungu ameneyu. Ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha kodi?”+
7 “N’chifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyoza Mulungu ameneyu. Ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha kodi?”+