Mateyu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, chapafupi n’chiti, kunena kuti, Machimo ako akhululukidwa, kapena kunena kuti, Nyamuka uyende?+ Maliko 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chapafupi n’chiti, kuuza wakufa ziwaloyu kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo nyamula machira ako uyende’?+
5 Mwachitsanzo, chapafupi n’chiti, kunena kuti, Machimo ako akhululukidwa, kapena kunena kuti, Nyamuka uyende?+
9 Chapafupi n’chiti, kuuza wakufa ziwaloyu kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo nyamula machira ako uyende’?+