Mateyu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake. Maliko 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi ina Yesu anali kudya patebulo m’nyumba ya Levi, ndipo okhometsa msonkho+ ndi ochimwa ambiri anali kudya pamodzi ndi iye ndi ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri ndipo anayamba kumutsatira.+ Luka 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano okhometsa msonkho+ komanso anthu ochimwa,+ onse anali kubwera kwa iye kudzamumvetsera.
10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake.
15 Pa nthawi ina Yesu anali kudya patebulo m’nyumba ya Levi, ndipo okhometsa msonkho+ ndi ochimwa ambiri anali kudya pamodzi ndi iye ndi ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri ndipo anayamba kumutsatira.+