Mateyu 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simunawerenge zimene Davide anachita atamva njala pamodzi ndi amuna omwe anali naye?+ Maliko 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yesu anati: “Kodi simunawerengepo zimene Davide+ pamodzi ndi amuna amene anali naye anachita atamva njala, alibiretu chilichonse?+
3 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simunawerenge zimene Davide anachita atamva njala pamodzi ndi amuna omwe anali naye?+
25 Koma Yesu anati: “Kodi simunawerengepo zimene Davide+ pamodzi ndi amuna amene anali naye anachita atamva njala, alibiretu chilichonse?+